Yesaya 14:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwe watayidwa kunja kwa manda ako, ngati nthambi yonyansa, ngati cobvala ca ophedwa, opyozedwa ndi lupanga, otsikira ku miyala ya dzenje, monga ngati mtembo wopondedwa ndi phazi.

Yesaya 14

Yesaya 14:15-24