Yesaya 14:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo amene akuona iwe adzayang'anitsitsa iwe, nadzalingalira za iwe, ndi kuti, Kodi uyu ndi munthu amene ananthunthumiritsa dziko lapansi, amene anagwedeza maufumu;

Yesaya 14

Yesaya 14:10-24