Yesaya 13:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo adzaopa; zowawa ndi masauko zidzawagwira; ndipo adzamva zowawa, ngati mkazi wakubala; adzazizwa wina ndi wina; nkhope zao zidzanga malawi a moto.

Yesaya 13

Yesaya 13:3-16