Yesaya 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuwani inu; pakuti tsiku la Yehova liri pafupi; lidzafika monga cionongeko cocokera kwa Wamphamvuyonse.

Yesaya 13

Yesaya 13:4-8