Yesaya 13:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau a khamu m'mapiri, akunga amtundu waukuru wa anthu, mau a phokoso la maufumu a mitundu yosonkhanidwa! Yehova wa makamu asonkhanitsa khamu kunkhondo.

Yesaya 13

Yesaya 13:1-8