Yesaya 13:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma zirombo za m'cipululu zidzagona pamenepo; nyumba zao zidzadzala ndi zakukuwa; ndipo nthiwatiwa zidzakhala pamenepo, ndipo atonde adzajidimuka pamenepo,

Yesaya 13

Yesaya 13:14-22