Yesaya 13:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndidzanthunthumiritsa miyamba, ndipo dziko lapansi lidzagwedezeka kucokera m'malo ace, m'mkwiyo wa Yehova wa makamu, tsiku la mkwiyo wace waukali.

Yesaya 13

Yesaya 13:6-16