Yesaya 12:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lomwelo mudzati, Muyamikire Yehova, bukitsani dzina lace, mulalikire macitidwe ace mwa mitundu ya anthu, munene kuti dzina lace lakwezedwa.

Yesaya 12

Yesaya 12:1-6