Yesaya 11:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo mzimu wa Yehova udzambalira iye mzimu wanzeru ndi wakuzindikira, mzimu wa uphungu ndi mphamvu, mzimu wakudziwa ndi wakuopa Yehova;

Yesaya 11

Yesaya 11:1-3