Yesaya 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nsanje ya Efraimu idzacoka, ndi iwo amene abvuta Yuda adzadulidwa; Efraimu sacitira nsanje Yuda, ndi Yuda sacitira nsanje Efraimu.

Yesaya 11

Yesaya 11:11-16