Yesaya 10:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Ambuye, Yehova wa makamu, adzarumiza kuonda mwa onenepa ace; ndipo pansi pa ulemerero wace padzayaka kutentha, konga ngati kutentha kwa moto.

Yesaya 10

Yesaya 10:12-19