Yesaya 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akadapanda Yehova wa makamu kutisiyira otsala ang'onong'ono ndithu, ife tikanakhala ngati Sodomu, ife tikadanga Gomora.

Yesaya 1

Yesaya 1:6-15