Yesaya 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dziko lanu liri bwinja; midzi yanu yatenthedwa ndi moto; dziko lanu alendo alimkudya pamaso panu; ndipo liri labwinja monga lagubuduzidwa ndi alendo.

Yesaya 1

Yesaya 1:2-11