Yesaya 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Imvani, miyamba inu, chera makutu, iwe dziko lapansi, cifukwa Yehova wanena, Ndakulitsa ndipo ndalera ana, ndipo iwo anandipandukira Ine.

Yesaya 1

Yesaya 1:1-12