Yesaya 1:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku anu okhala mwezi ndi nthawi za mapwando anu mtima wanga uzida; zindibvuta Ine; ndalema ndi kupirira nazo.

Yesaya 1

Yesaya 1:9-22