Yeremiya 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo apinda lilime lao ngati uta wao, liname; koma akula mphamvu m'dzikomo, koma si pacoonadi; pakuti alinkunkabe nacita zoipa, ndipo sandidziwa Ine, ati Yehova.

Yeremiya 9

Yeremiya 9:1-13