Yeremiya 9:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzawabalalitsanso mwa amitundu, amene iwo kapena makolo ao sanawadziwa; ndipo ndidzatumiza lupanga, liwatsate mpaka ndawatha.

Yeremiya 9

Yeremiya 9:6-22