Yeremiya 8:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndidzapereka akazi ao kwa ena, ndi minda yao kwa iwo adzalowamo; pakuti onse kuyambira wamng'ono kufikira wamkuru asirirasirira; kuyambira mneneri kufikira wansembe onse acita zonyenga.

Yeremiya 8

Yeremiya 8:1-18