Yeremiya 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi yomweyo, ati Yehova, adzaturutsa m'manda mwao mafupa a mafumu a Yuda, ndi mafupa a akuru ace, ndi mafupa a ansembe, ndi mafupa a aneneri, ndi mafupa a okhala m'Yerusalemu,

Yeremiya 8

Yeremiya 8:1-4