Yeremiya 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lalikirani nkhondo yakumenyana ndi iye; ukani, tikwere pakati pa usana. Tsoka kwa ife! pakuti dzuwa lapendeka, mithunzi ya madzulo yatambasuka.

Yeremiya 6

Yeremiya 6:1-5