Yeremiya 6:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, udzibveke ndi ciguduli, ndi kubvimbvinika m'phulusa; ulire maliro ngati a mwana wamwamuna wa yekha, kulira kowawa koposa; pakuti wakufunkha adzatifikira ife motidzidzimutsa.

Yeremiya 6

Yeremiya 6:23-30