Yeremiya 6:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi anakhala ndi manyazi pamene anacita conyansa? lai, sanakhala konse ndi manyazi, sanathe kunyala; cifukwa cace adzagwa mwa iwo akugwa; panthawi pamene ndidzafika cwa iwo, aclzagwetsedwa, ati Yehova.

Yeremiya 6

Yeremiya 6:7-19