Yeremiya 52:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

caka ca makumi awiri ndi zitatu ca Nebukadirezara Nebuzaradani kapitao wa alonda anatenga ndende Ayuda mazana asanu ndi awiri kudza makumi anai ndi asanu; anthu onse anali zikwi zinai kudza mazana asanu ndi limodzi.

Yeremiya 52

Yeremiya 52:26-32