Yeremiya 52:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti zonse zinacitika m'Yerusalemu ndi m'Yuda cifukwa ca mkwiyo wa Yehova, mpaka anawacotsa pamaso pace; ndipo Zedekiya anampandukira mfumu ya Babulo.

Yeremiya 52

Yeremiya 52:1-5