Yeremiya 52:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya ku Babulo anawakantha, nawapha pa Ribila m'dziko la Hamati. Comweco Yuda anatengedwa ndende kuturuka m'dziko lace.

Yeremiya 52

Yeremiya 52:18-31