Yeremiya 52:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zedekiya anali wa zaka makumi awiri kudza cimodzi pamene analowa ufumu wace; ndipo analamulira m'Yerusalemu zaka khumi kudza cimodzi; dzina la amace ndi Hamutala mwana wamkazi wa Yeremiya wa ku Libina.

Yeremiya 52

Yeremiya 52:1-3