Yeremiya 51:59 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amene Yeremiya mneneri anauza Seraya mwana wa Neriya, mwana wa Maseya, pamene iye ananka ndi Zedekiya mfumu ya Yuda ku Babulo caka cacinai ca ufumu wace. Ndipo Seraya anali kapitao wa cigono cace.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:57-64