Yeremiya 51:56 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti wakufunkha wafika kwa iye, kwa Babulo, ndi anthu ace olimba agwidwa, mauta ao atyokatyoka, pakuti Yehova ndiye Mulungu wakubwezera, adzabwezera ndithu.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:48-59