Yeremiya 51:53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngakhale Babulo adzakwera kumwamba, ngakhale adzalimbitsa msanje wa mphamvu yace, koma kucokera kwa Ine akufunkha adzafika kwa iye, ati Yehova.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:43-62