Yeremiya 51:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamene Iye anena mau, pali unyinji wa madzi m'mwamba, ndipo akweretsa nkhungu ku malekezero a dziko lapansi, ayesa mphezi ya mvula, aturutsa mphepo ya m'nyumba za cuma zace.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:15-20