Yeremiya 50:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tamvani uphungu wa Yehova, umene waupangira pa Babulo; ndi zimene walingirira dziko la Akasidi; ndithu adzawakoka, ana ang'ono a zoweta; ndithu adzayesa busa lao bwinja pamodzi nao.

Yeremiya 50

Yeremiya 50:38-46