Yeremiya 50:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, nditsutsana nawe, wonyada iwe, ati Ambuye, Yehova wa makamu; pakuti tsiku lako lafika, nthawi imene ndidzakulanga iwe.

Yeremiya 50

Yeremiya 50:30-32