Yeremiya 50:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova watsegula pa nyumba ya zida zace, ndipo waturutsa zida za mkwiyo wace; pakuti Ambuye Yehova wa makamu, ali ndi nchito m'dziko la Akasidi.

Yeremiya 50

Yeremiya 50:24-28