Yeremiya 50:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kwera kukamenyana ndi dziko la Merataimu, ndi okhala m'Pekoli, ipha nuononge konse pambuyo pao, ati Yehova, cita monga mwa zonse ndinakuuza iwe.

Yeremiya 50

Yeremiya 50:18-30