Yeremiya 50:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa mukondwa, cifukwa musekerera, inu amene mulanda colowa canga, cifukwa muli onenepa monga ng'ombe yamsoti yoponda tirigu, ndi kulira ngati akavalo olimba;

Yeremiya 50

Yeremiya 50:5-20