Yeremiya 5:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Codabwitsa ndi coopsya caoneka m'dzikomo;

31. aneneri anenera monyenga nathandiza ansembe pakulamulira kwao; ndipo anthu anga akonda zotere; ndipo mudzacita ciani pomarizira pace?

Yeremiya 5