Yeremiya 5:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova Inu, maso anu sali pacoonadi kodi? munawapanda iwo, koma sanaphwetekedwa mtima; munawatha iwo, koma akana kudzudzulidwa; alimbitsa nkhope zao koposa mwala; akana kubwera.

Yeremiya 5

Yeremiya 5:1-4