Yeremiya 5:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo sanena m'mtima mwao, Tiopetu Yehova Mulungu wathu wopatsa mvula yoyamba ndi yamasika, m'nyengo yace; atisungira ife masabata olamulidwa a masika.

Yeremiya 5

Yeremiya 5:22-27