Yeremiya 49:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa canji udzitamandira ndi zigwa, cigwa cako coyendamo madzi, iwe mwana wamkazi wobwerera m'mbuyo, amene anakhulupirira cuma cace, nati, Adza kwa ine ndani?

Yeremiya 49

Yeremiya 49:1-9