Yeremiya 49:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Thawani inu, yendani kutari, khalani mwakuya, Inu okhala m'Hazori, ati Yehova; pakuti Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo anapangira uphungu pa inu, nakulingalirirani.

Yeremiya 49

Yeremiya 49:22-36