Yeremiya 49:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Za Kedara, ndi za maufumu a Hazori, amene anawakantha Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo.Yehova atero: Ukani, kwerani ku Kedara, funkhani ana a kum'mawa.

Yeremiya 49

Yeremiya 49:19-30