Yeremiya 49:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Za Damasiko. Hamati ndi Aripadi ali ndi manyazi, cifukwa anamva malodza, asungunuka kunyanja, adera nkhawa osatha kukhala cete.

Yeremiya 49

Yeremiya 49:13-25