Yeremiya 49:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndalumbira, Pali Ine, ati Yehova, kuti Boma adzakhala cizizwitso, citonzo, copasuka, ndi citemberero; ndipo midzi yace yonse idzakhala yopasuka cipasukire.

Yeremiya 49

Yeremiya 49:3-16