Yeremiya 48:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndidzabwezanso undende wa Moabu masiku akumariza, ati Yehova. Ziweruzo za Moabu ndi zomwezi.

Yeremiya 48

Yeremiya 48:44-47