Yeremiya 48:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace mtima wanga umlima Moabu monga zitolilo, ndipo mtima wanga uwalirira anthu a Kireresi monga zitolilo, cifukwa cace zakucuruka zace adadzionera zatayika.

Yeremiya 48

Yeremiya 48:31-37