Yeremiya 48:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kusekera ndi kukondwa kwacotsedwa, ku munda wobala ndi ku dziko la Moabu; ndipo ndaletsa vinyo pa zoponderamo; sadzaponda ndi kupfuula; kupfuula sikudzakhala kupfuula.

Yeremiya 48

Yeremiya 48:24-43