Yeremiya 48:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ife tamva kudzikuza kwa Moabu, wadzikuza ndithu, kunyang'wa kwace, ndi kunyada kwace, ndi kudzitama kwace, ndi kudzikuza kwa mtima wace.

Yeremiya 48

Yeremiya 48:25-33