Yeremiya 48:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Moabu wapasuka, akwera kulowa m'midzi yace, ndi anyamata ace osankhika atsikira kukaphedwa, ati Mfumu, dzina lace ndiye Yehova wa makamu.

Yeremiya 48

Yeremiya 48:7-24