Yeremiya 48:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Moabu wakhala m'mtendere kuyambira ubwana wace, wakhala pansenga, osatetekulidwa, sananke kundende; cifukwa cace makoleredwe ace alimobe mwa iye, pfungo lace silinasinthika.

Yeremiya 48

Yeremiya 48:3-16