Yeremiya 46:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzawapereka m'manja a iwo amene afuna moyo wao, ndi m'dzanja la Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo, ndi m'manja a atumiki ace; pambuyo pace adzakhalamo anthu, monga masiku akale, ati Yehova.

Yeremiya 46

Yeremiya 46:23-28